Onani zimene zilipo

DECEMBER 2, 2022
NKHANI ZA PADZIKO LONSE

Ciunikilo Na. 8 ca Bungwe Lolamulila mu 2022

Ciunikilo Na. 8 ca Bungwe Lolamulila mu 2022

Wa m’Bungwe Lolamulila akutilimbikitsa kukhala okonzeka kusintha galeta la Yehova likamayenda. Akutithandizanso kuona mapindu a misonkhano ya pamaso-m’pamaso.