Pitani ku nkhani yake

Insayikulopediya ya Baibulo

Insayikulopediya ya Baibulo

Buku lachingelezi la Insight on the Scriptures ndi Insayikulopediya ya Baibulo yomwe ingakuthandizeni kuphunzira mozama nkhani za m’Baibulo. Bukuli lingakuthandizeni kwambiri pophunzira Baibulo chifukwa limafotokoza mawu masauzande ambiri okhudza zinthu monga izi:

  • anthu

  • malo

  • zomera

  • zinyama

  • zochitika zofunika

  • mawu ophiphiritsa a m’Baibulo

  • makhalidwe

  • mawu a m’chilankhulo chimene Baibulo linalembedwa

  • buku lililonse la m’Baibulo

Mungapeze bukuli kwaulere pa intaneti kapena mungapange dawunilodi PDF ya mavoliyumu onse awiri a bukuli.