ZOTI MUCHITE Kuonjezera Anzanga YAMBANI Zoti muchitezi zikuthandizani kuti mukhale ndi anzanu a misinkhu yosiyanasiyana. Pangani Dawunilodi Nkhani Zina Zoti Achinyamata Achite Achinyamata Mwina Mungakondenso Kudziwa Izi ZIMENE ACHINYAMATA AMAFUNSA Kodi Ndiwonjezere Anzanga? Zimakhala bwino kukhala ndi kagulu kochepa ka anzanu, koma sikuti zimenezi zimathandiza nthawi zonse. N’chifukwa chiyani? MAVIDIYO AMAKATUNI Kodi Mnzako Weniweni Ungamudziwe Bwanji? N’zosavuta kupeza anzanu amene sangakuthandizeni, koma kodi mungapeze bwanji mnzanu weniweni? KUYANKHA MAFUNSO A M’BAIBULO Kodi Baibulo Limati Chiyani pa Nkhani Yokhala ndi Anzathu? Anzathu abwino angatithandize kukhala anthu abwino. Tiyenera kusankha anzathu mwanzeru. GALAMUKANI! Kodi Mungatani Kuti Mukhale ndi Anzanu Apamtima? Mfundo 4 zomwe zingakuthandizeni kuti mupeze anzanu apamtima. GALAMUKANI! Kodi Mungatani Kuti Mukhale Bwenzi Labwino? Anthu ambiri amaona kuti kukhala ndi mabwenzi n’kofunika. Kodi mungatani kuti mukhale bwenzi labwino? Nkhaniyi ikufotokoza mfundo 4 za m’Baibulo zomwe zingakuthandizeni. GALAMUKANI! Kodi Ndingadziwe Bwanji Anzanga Enieni? Patsani ena Patsani ena Kuonjezera Anzanga ZOTI ACHINYAMATA ACHITE Kuonjezera Anzanga Chichewa Kuonjezera Anzanga https://cms-imgp.jw-cdn.org/img/p/502017117/univ/art/502017117_univ_sqr_xl.jpg