Mboni za Yehova Padziko Lonse

Madagascar

Mfundo Zachidule—Madagascar

  • 29,443,000—Chiwerengero cha anthu
  • 40,035—Chiwerengero cha Mboni za Yehova
  • 841—Mipingo
  • Pa anthu 763 alionse pali wa Mboni za Yehova m’modzi

NSANJA YA OLONDA (YOPHUNZIRA)

Anadzipereka ndi Mtima Wonse ku Madagascar

Werengani nkhaniyi kuti mudziwe za anthu amene adzipereka kuti akathandize kufalitsa uthenga wa Ufumu kumadera osiyanasiyana a m’dziko lalikulu la Madagascar.