Mboni za Yehova Padziko Lonse

Norway

  • Finnmarksvidda, Norway—Akulalikira m’dera la anthu a Chisami

  • Ranheim, Norway—Akusonyeza vidiyo yakuti N’chifukwa Chiyani Tiyenera Kuphunzira Baibulo? ndipo mumlengalenga mukuoneka kuwala kokongola

  • Finnmarksvidda, Norway—Akulalikira m’dera la anthu a Chisami

  • Ranheim, Norway—Akusonyeza vidiyo yakuti N’chifukwa Chiyani Tiyenera Kuphunzira Baibulo? ndipo mumlengalenga mukuoneka kuwala kokongola

Mfundo Zachidule—Norway

  • 5,504,000—Chiwerengero cha anthu
  • 12,034—Chiwerengero cha Mboni za Yehova
  • 162—Mipingo
  • Pa anthu 464 alionse pali wa Mboni za Yehova m’modzi

NSANJA YA OLONDA (YOPHUNZIRA)

Anadzipereka ndi Mtima Wonse ku Norway

Kodi funso limene anafunsidwa mosayembekezereka linathandiza bwanji banja lina kuti lisamukire kudera limene kukufunika anthu ambiri ogwira ntchito yolalikira?