Mboni za Yehova Padziko Lonse

Indonesia

  • Bali, Indonesia—Akuphunzira Baibulo ndi mlimi wa mpunga pafupi ndi tawuni ya Ubud

Mfundo Zachidule—Indonesia

  • 281,844,000—Chiwerengero cha anthu
  • 31,023—Chiwerengero cha Mboni za Yehova
  • 491—Mipingo
  • Pa anthu 9,275 alionse pali wa Mboni za Yehova m’modzi

Buku Lapachaka la Mboni za Yehova la 2016

Indonesia

A Mboni za Yehova analimba mtima pamene ankakumana ndi mavuto chifukwa cha kusintha kwa zinthu pa nkhani zandale, mikangano ya zipembedzo, komanso kuletsedwa kwa ntchito yawo kwa zaka 25 kumene atsogoleri azipembedzo anachititsa.

NKHANI

Mavuto Apadziko Lonse: Kuthandiza Abale Athu Pakachitika Ngozi

Bungwe Lolamulira lipitirizabe kuthandiza mofulumira komanso kupereka malangizo kwa abale ndi alongo athu omwe akhudzidwa ndi mliri wa kolonavairasi.

KALE LATHU

Boti la Lightbearer Linabweretsa Kuwala kwa Choonadi Kum’mwera Chakum’mawa kwa Asia

Ngakhale kuti ankatsutsidwa, amuna ochepa a m’boti la Lightbearer anafalitsa molimba mtima kuwala kwa choonadi cha m’Baibulo m’dera lalikulu kwambiri lokhala anthu ambiri.

GALAMUKANI!

Dziko la Indonesia

Werengani kuti mudziwe za chikhalidwe ndi miyambo ya anthu ochezeka, oleza mtima komanso okonda kuchereza alendo.