Mboni za Yehova Padziko Lonse

Ghana

  • Aburi, Ghana—Akulalikira za Ufumu wa Mulungu

Mfundo Zachidule—Ghana

  • 33,063,000—Chiwerengero cha anthu
  • 153,657—Chiwerengero cha Mboni za Yehova
  • 2,484—Mipingo
  • Pa anthu 220 alionse pali wa Mboni za Yehova m’modzi

NSANJA YA OLONDA (YOPHUNZIRA)

Anadzipereka ndi Mtima Wonse—Ku Ghana

Anthu amene anasamukira m’mayiko ena amakumana ndi mavuto ambiri koma amadalitsidwanso kwabasi.