Mboni za Yehova Padziko Lonse

Burkina Faso

  • Manga, Burkina Faso—Akulalikira pa nthawi yokolola thonje

Mfundo Zachidule—Burkina Faso

  • 22,721,000—Chiwerengero cha anthu
  • 1,986—Chiwerengero cha Mboni za Yehova
  • 50—Mipingo
  • Pa anthu 12,470 alionse pali wa Mboni za Yehova m’modzi

NSANJA YA OLONDA (YOPHUNZIRA)

Anadzipereka ndi Mtima Wonse Kumadzulo kwa Africa

Kodi n’chiyani chinalimbikitsa Akhristu ena ku Ulaya kuti asamukire kumadzulo kwa Africa, nanga zinthu zikuwayendera bwanji kumeneko?

NSANJA YA OLONDA (YOPHUNZIRA)

Kuyandikira kwa Mulungu Ndi Kwabwino

Sarah Maiga anasiya kukula ali ndi zaka 9 koma akutumikira Yehova mwakhama.