Pitani ku nkhani yake

Zimene Zili Muvidiyo Yakuti: Moyo wa Yesu Komanso Utumiki Wake: Vidiyo Yoyamba​—Kuwala Kwenikweni kwa Dziko

Zimene Zili Muvidiyo Yakuti: Moyo wa Yesu Komanso Utumiki Wake: Vidiyo Yoyamba​—Kuwala Kwenikweni kwa Dziko

Yehova akufotokoza mmene adzapulumutsire mtundu wonse wa anthu. Mngelo akuuza Zekariya yemwe ndi wachikulire kuti iye limodzi ndi mkazi wake Elizabeti, adzabereka mwana yemwe adzakhale mneneri. Yosefe ndi Mariya adzalera Mesiya ndipo akuyenera kuteteza mwanayo kwa adani.