Pitani ku nkhani yake

Mukuitanidwa ku Msonkhano wa Mboni za Yehova wa 2024 Wakuti ‘Lalikirani Uthenga Wabwino’

Mukuitanidwa ku Msonkhano wa Mboni za Yehova wa 2024 Wakuti ‘Lalikirani Uthenga Wabwino’

Uthenga woipa ungatifooketse, koma uthenga wabwino ukhoza kutithandiza kuti tiziona kuti zinthu zidzayamba kuyenda bwino m’tsogolomu.