Kondwelani na Moyo Kwamuyaya!—Maphunzilo a Baibo Oyambilapo

Kabuku kano ni poyambila cabe pa phunzilo lanu la Baibo monga mbali ya pulogilamu yathu yophunzitsa Baibo kwaulele.

Mungakondenso Izi

MAFUNSO AMENE AMAFUNSIDWA KAŴILI-KAŴILI

Kodi Phunzilo la Baibulo N’ciani?

Pezani mayankho a mafunso okhudza mmene timacitila phunzilo la Baibulo laulele.