Tsegulani ndi kuwerenga nkhani zokhala ndi mitu yokhudza Baibulo, mmene lingatithandizire, komanso zochitika zosiyanasiyana zokhudza a Mboni za Yehova. Sankhani chinenero chomwe mukufuna pakabokosi kosankhira chinenero kuti muone nkhani zosiyanasiyana zomwe zikupezeka m’chinenerocho.
NKHANI ZINA
Mulungu amaona kuti akazi ayenera kutetezedwa. Onani chifukwa chake amaona choncho komanso zimene adzachite pothetsa nkhanza zonse zimene anthu amachitira akazi.
NKHANI ZINA
Mulungu amaona kuti akazi ayenera kutetezedwa. Onani chifukwa chake amaona choncho komanso zimene adzachite pothetsa nkhanza zonse zimene anthu amachitira akazi.