Onani zimene zilipo

Kuwala na Mitundu

Kuwala na Mitundu

M’dziko lathuli muli mitundu yosiyana-siyana. Dziŵani amene ali gwelo la kuwala na mitundu, ndiponso mmene kuwala na mitundu kumaonetsela luso la amene anakupanga.