Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

Kodi Yesu Khristu ni Mulungu?

Kodi Yesu Khristu ni Mulungu?

Anthu ambili amaona kuti Yesu ni munthu amene zocita zake zinakhudza anthu ambili. Koma kodi Yesu ndiye Mulungu Wamphamvuzonse? Kapena anali cabe munthu wabwino?