NSANJA YA MLONDA—YOPHUNZILA April 2024

Magazini ino ili na nkhani zophunzila mu mlungu wa June 10–​July 7, 2024.

NKHANI YOPHUNZILA 14

“Tiyesetse Mwakhama Kuti Tikhale Okhwima Mwauzimu”

Yophunzila mu mlungu wa June 10-16, 2024.

NKHANI YOPHUNZILA 15

Kulitsani Ciyamikilo Canu pa Gulu la Yehova

Yophunzila mu mlungu wa June 17-23, 2024.

NKHANI YOPHUNZILA 16

Mmene Tingaonjezele Cimwemwe Cathu mu Ulaliki

Yophunzila mu mlungu wa June 24-30, 2024.

NKHANI YOPHUNZILA 17

Musacokemo m’Paradaiso Wauzimu

Yophunzila mu mlungu wa July 1-7, 2024.

MBILI YANGA

Zifooko Zanga Zaonetsa Mphamvu za Mulungu

M’bale Erkki Mäkelä akufotokoza mmene Yehova anam’thandizila kuthana na zovuta pamene anali mu utumiki wa nthawi zonse, komanso pomwe anali kutumikila monga m’mishonale m’madela a ku Columbia komwe kunali kucitika zaciwawa cifukwa ca asilikali oukila boma.

Kodi Mudziŵa?

N’cifukwa ciyani amuna amene sanali Aisiraeli anatumikila m’gulu la asilikali a Mfumu Davide?