Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

GALAMUKA! Na. 2 2021 | Kodi Ndinu Kapolo wa Zipangizo Zamakono?

Kodi ndinu kapolo wa zipangizo zamakono? Anthu ambili amakamba kuti amakwanitsa kuseŵenzetsa bwino zipangizo zawo. Koma zipangizo zamakono zingabweletse mavuto amene anthu sangawazindikile.

Kodi Zipangizo Zamakono Zimakhudza Bwanji Ubwenzi Wanu na Ena?

Zipangizo zamakono zingakuthandizeni pokambilana na mabwenzi anu na kulimbitsa ubwenziwo.

Kodi Zipangizo Zamakono Zimawakhudza Bwanji Ana Anu?

Ngakhale kuti ana savutika kuseŵenzetsa zipangizo zamakono, amafunikabe thandizo.

Kodi Zipangizo Zamakono Zimakhudza Bwanji Cikwati Canu?

Ngati mwamuna na mkazi wake amaseŵenzetsa bwino zipangizo zamakono, zingawathandize kulimbitsa mgwilizano wawo.

Kodi Zipangizo Zamakono Zimakhudza Bwanji Luso Lanu Lophunzila Zinthu?

Zingakhudze luso lanu lomvetsa zinthu poŵelenga, komanso mmene mumaonela nthawi yokhala nokha, ndipo zingakhulepheletseni kuika maganizo pa cinthu cimodzi. Zinthu zitatu zimene mungacite kuti munole luso lanu lophunzila zinthu.

Phunzilani Zambili pa JW.ORG

Ni nkhani iti imene mungakonde kuiŵelenga?

Za M’kope Ino

Onani njila zovuta kuzizindikila koma zowononga zoonetsa mmene zipangizo zamakono zingakhudzile ubwenzi wanu na ena, banja lanu, ndiponso ngakhale luso lanu lophunzila zinthu.