Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

Uthenga Wabwino Wolembedwa na Maliko

Macaputala

1 2 3 4 5 6 7 8 9 10 11 12 13 14 15 16

Za m'Bukuli

  • 1

    • Ulaliki wa Yohane M’batizi (1-8)

    • Ubatizo wa Yesu (9-11)

    • Yesu ayesedwa na Satana (12, 13)

    • Yesu ayamba kulalikila ku Galileya (14, 15)

    • Yesu aitana ophunzila ake oyamba (16-20)

    • Yesu atulutsa mzimu wonyansa (21-28)

    • Yesu acilitsa anthu ambili ku Kaperenao (29-34)

    • Apemphela kwayekha (35-39)

    • Wakhate acilitsidwa (40-45)

  • 2

    • Yesu acilitsa munthu wakufa ziwalo (1-12)

    • Yesu aitana Levi (13-17)

    • Funso pa nkhani ya kusala kudya (18-22)

    • Yesu, ‘Mbuye wa Sabata’ (23-28)

  • 3

    • Munthu wa dzanja lopuwala acilitsidwa (1-6)

    • Khamu lalikulu la anthu m’mbali mwa nyanja (7-12)

    • Atumwi 12 (13-19)

    • Kunyoza mzimu woyela (20-30)

    • Mayi a Yesu na abale ake (31-35)

  • 4

    • MAFANIZO ONENA ZA UFUMU (1-34)

      • Wofesa mbewu (1-9)

      • Cifukwa cake Yesu anaseŵenzetsa mafanizo (10-12)

      • Kufotokoza tanthauzo la fanizo la wofesa mbewu (13-20)

      • Nyale saibwinikila na thadza (21-23)

      • Muyeso umene mukupimila ena (24, 25)

      • Wofesa mbewu amene amagona (26-29)

      • Kanjele ka mpilu (30-32)

      • Kuseŵenzetsa mafanizo (33, 34)

    • Yesu aleketsa cimphepo camkuntho (35-41)

  • 5

    • Yesu atumiza ziŵanda m’nkhumba (1-20)

    • Mwana wamkazi wa Yairo; mzimayi agwila covala cakunja ca Yesu (21-43)

  • 6

    • Yesu akanidwa mu mzinda wa kwawo (1-6)

    • Atumwi 12 apatsidwa malangizo a ulaliki (7-13)

    • Imfa ya Yohane M’batizi (14-29)

    • Yesu adyetsa anthu 5,000 (30-44)

    • Yesu ayenda pa madzi (45-52)

    • Acilitsa anthu ku Genesareti (53-56)

  • 7

    • Kuvumbula miyambo ya anthu (1-13)

    • Zodetsa munthu zimacokela mu mtima (14-23)

    • Cikhulupililo ca mayi wacisirofoinike (24-30)

    • Munthu wogontha acilitsidwa (31-37)

  • 8

    • Yesu adyetsa anthu 4,000 (1-9)

    • Apempha cizindikilo (10-13)

    • Zofufumitsa za Afarisi na za Herode (14-21)

    • Munthu wakhungu acilitsidwa ku Betsaida (22-26)

    • Petulo azindikila Khristu (27-30)

    • Yesu anenelatu za imfa yake (31-33)

    • Zimene ophunzila oona a Yesu amacita (34-38)

  • 9

    • Kusandulika kwa Yesu (1-13)

    • Kamnyamata kogwidwa na ciŵanda kacilitsidwa (14-29)

      • Zinthu zonse n’zotheka kwa munthu wacikhulupililo (23)

    • Yesu akambilatunso za imfa yake (30-32)

    • Ophunzila akangana zakuti wamkulu ndani (33-37)

    • Aliyense amene satsutsana nafe ali ku mbali yathu (38-41)

    • Zopunthwitsa (42-48)

    • “Khalani na mcele mwa inu” (49, 50)

  • 10

    • Ukwati na cisudzulo (1-12)

    • Yesu adalitsa ana (13-16)

    • Funso la munthu wacuma (17-25)

    • Kudzimana cifukwa ca Ufumu (26-31)

    • Yesu akambilatunso za imfa yake (32-34)

    • Pempho la Yakobo na Yohane (35-45)

      • Yesu ni dipo lowombolela anthu ambili (45)

    • Batimeyu wakhungu acilitsidwa (46-52)

  • 11

    • Yesu atamandidwa poloŵa mu Yerusalemu (1-11)

    • Atembelela mtengo wa mkuyu (12-14)

    • Yesu ayeletsa kacisi (15-18)

    • Phunzilo pa mtengo wa mkuyu wofota (19-26)

    • Ulamulilo wa Yesu utsutsidwa (27-33)

  • 12

    • Fanizo la alimi akupha (1-12)

    • Mulungu na Kaisara (13-17)

    • Funso pa nkhani ya kuuka kwa akufa (18-27)

    • Malamulo aŵili aakulu kwambili (28-34)

    • Kodi Khristu ni mwana wa Davide? (35-37a)

    • Yesu acenjeza anthu za alembi (37b-40)

    • Tumakobili tuŵili twa mkazi wamasiye wosauka (41-44)

  • 13

    • CIMALIZILO CA NTHAWI INO (1-37)

      • Nkhondo, zivomezi, njala (8)

      • Uthenga wabwino udzalalikidwa (10)

      • Cisautso cacikulu (19)

      • Kubwela kwa Mwana wa munthu (26)

      • Fanizo la mtengo wa mkuyu (28-31)

      • Khalanibe maso (32-37)

  • 14

    • Ansembe akonza ciwembu cakuti aphe Yesu (1, 2)

    • Yesu athilidwa mafuta onunkhila (3-9)

    • Yudasi apeleka Yesu (10, 11)

    • Pasika wothela (12-21)

    • Kukhazikitsa Mwambo wa Mgonelo wa Ambuye (22-26)

    • Yesu akambilatu kuti Petulo adzamukana (27-31)

    • Yesu apemphela pa malo ochedwa Getsemani (32-42)

    • Yesu agwidwa (43-52)

    • Yesu azengedwa mlandu m’Khoti Yaikulu ya Ayuda (53-65)

    • Petulo akana Yesu (66-72)

  • 15

    • Yesu aonekela pamaso pa Pilato (1-15)

    • Yesu acitidwa zacipongwe pamaso pa anthu (16-20)

    • Amukhomelela pa mtengo ku Gologota (21-32)

    • Imfa ya Yesu (33-41)

    • Yesu aikidwa m’manda (42-47)

  • 16

    • Yesu aukitsidwa (1-8)