Mmene Mungaigwiritsire Ntchito pa Windows 8 Kapena pa Windows Phone 8
JW Library ndi pulogalamu yovomerezeka imene inapangidwa ndi a Mboni za Yehova. Pulogalamuyi ili ndi Mabaibulo osiyanasiyana komanso mabuku ndi timabuku tothandiza pophunzira Baibulo.
M'CHIGAWO ICHI
Mmene Mungaikire JW Library M’chipangizo Chanu Ngati Simukuipeza ku App Store—Windows
Ngati simungathe kuika JW Library m’chipangizo chanu chokhala ndi pulogalamu ya Windows pa app store yovomerezeka, mukhoza kuika nokha pogwiritsa ntchito mafailo a Windows oikira JW Library.
Mafunso Ofunsidwa Kawirikawiri Okhudza JW Library (Pa Zipangizo za Windows)
Pezani mayankho a mafunso ofunsidwa kawirikawiri.