Pitani ku nkhani yake

Makadi a Anthu Otchulidwa M’Baibulo

Dziwani nkhani za anthu osiyanasiyana amene amakuchititsani chidwi otchulidwa m’Baibulo. Koperani khadi lililonse, lisindikizeni, lipindeni pakati ndi kulisunga. Koperani ndi kusunga makadi onse.