Pitani ku nkhani yake

Zoti Muchite Pophunzira Baibulo

Tetezani Kulambira Koona

Mungaphunzire zambiri pa nkhani ya Eliya. Koperani nkhani ya m’Baibuloyi, iwerengeni, ndipo muiganizire mozama n’kuona mmene ingakuthandizireni.