Pitani ku nkhani yake

Eritrea

 

A Mboni za Yehova ku Eritrea

● A Mboni Anamangidwa Chifukwa cha Chikhulupiriro Chawo​—???

2018-06-06

ERITREA

A Mboni za Yehova Awiri Achikulire Anafera M’ndende ku Eritrea

A Habtemichael Tesfamariam ndi a Habtemichael Mekonen anafera m’ndende ya Mai Serwa chakumayambiriro kwa chaka cha 2018. A Mboniwa anamangidwa ndi kuikidwa m’ndende mopanda chilungamo chifukwa cha zimene amakhulupirira ndipo anakhala mozunzika m’ndendemo kwa zaka pafupifupi 10.

2014-10-10

ERITREA

Kodi Anthu Amene Atha Zaka 20 Ali M’ndende ku Eritrea Adzatuluka?

Azibambo atatu a Mboni atha zaka 20 ali m’ndende popanda kuimbidwa mlandu. Enanso ambiri ali m’ndende. Kodi dziko la Eritrea lidzasiya kuzunza anthu chifukwa cha chipembedzo chawo?

2016-12-22

ERITREA

Kwa Nthawi Yoyamba Mayiko Ambiri Asonyeza Kuti Sakugwirizana ndi Nkhanza Zimene Dziko la Eritrea Likuchitira a Mboni za Yehova

Gulu limene bungwe la United Nations linakhazikitsa linanena kuti “kumanga munthu pa zifukwa za chipembedzo kapena mtundu wake, n’kosemphana ndi malamulo omwe mayiko anakhazikitsa” komanso ndi mlandu wophwanya ufulu wa anthu.