Pitani ku nkhani yake

BAIBULO LIMASINTHA ANTHU

Kodi Chikondi Komanso Kukhulupirika Zidzagonjetsa Liti Chidani?

Kodi Chikondi Komanso Kukhulupirika Zidzagonjetsa Liti Chidani?

Ngakhale kuti Ayuda ndi anthu a ku Palesitina akhala akudana komanso kuchitirana zachiwawa kwa nthawi yaitali, anthu ena akwanitsa kusiya mtima wodana ndi anthu amtundu wina. Vidiyoyi ikufotokoza za anthu awiri amene anakwanitsa kuchita zimenezi.