Pitani ku nkhani yake

“Kaya Ndikanagwira Mtengo Wanji?”

“Kaya Ndikanagwira Mtengo Wanji?”

Onerani kavidiyoka kuti mumve zimene munthu wina wakhungu ananena poyamikira mmene Baibulo la zilembo za akhungu lamuthandizira.