Mboni za Yehova Padziko Lonse

Zimbabwe

  • M’boma la Matobo ku Zimbabwe—Akulalikira kunyumba ndi nyumba

Mfundo Zachidule—Zimbabwe

  • 15,179,000—Chiwerengero cha anthu
  • 48,748—Chiwerengero cha Mboni za Yehova
  • 961—Mipingo
  • Pa anthu 324 alionse pali wa Mboni za Yehova m’modzi

NSANJA YA OLONDA (YOPHUNZIRA)

Ndinalola Kuti Yehova Azinditsogolera pa Moyo Wanga

Mbiri ya Moyo Wanga: Keith Eaton

KODI ZOPEREKA ZANU ZIMAGWIRITSIDWA NTCHITO BWANJI?

Kuthandiza Anthu Amene Akhudzidwa Ndi Ngozi Zadzidzidzi

M’chaka chautumiki cha 2020, abale ndi alongo ambiri anakhudzidwa ndi mliri komanso ngozi zam’chilengedwe. Kodi tinawathandiza bwanji?