Mboni za Yehova Padziko Lonse

South Africa

  • Stellenbosch, South Africa—Akulalikira kwa mlimi wa mphesa pafupi ndi mzinda wa Cape Town

  • Ku Bo-Kaap mumzinda wa Cape Town ku South Africa—Akulalikira m’dera lina la mzindawu

  • Ku Weltevrede m’chigawo cha Mpumalanga ku South Africa—Akuitanira mzimayi woyankhula Chindebele ku misonkhano ya mpingo

Mfundo Zachidule—South Africa

  • 60,605,000—Chiwerengero cha anthu
  • 100,331—Chiwerengero cha Mboni za Yehova
  • 1,966—Mipingo
  • Pa anthu 617 alionse pali wa Mboni za Yehova m’modzi

NSANJA YA OLONDA (YOPHUNZIRA)

Ndakhala Ndikusangalala Kutumikira Yehova

Mbiri ya Moyo Wanga: John Kikot

KODI ZOPEREKA ZANU ZIMAGWIRITSIDWA NTCHITO BWANJI?

Tchanelo cha JW Setilaiti Chimaoneka Kumene Kulibe Intaneti

Kodi abale a ku Africa amatani kuti aonere JW Broadcasting ngati alibe intaneti?