Mboni za Yehova Padziko Lonse

Virgin Islands, British

Mfundo Zachidule—Virgin Islands, British

  • 31,000—Chiwerengero cha anthu
  • 222—Chiwerengero cha Mboni za Yehova
  • 4—Mipingo
  • Pa anthu 140 alionse pali wa Mboni za Yehova m’modzi

NKHANI

A Mboni Akugwira Mwakhama Ntchito Yothandiza Anthu Omwe Anakhudzidwa Ndi Mphepo Zamkuntho

Maofesi a Nthambi a Mboni za Yehova akufotokoza zimene akuchita pothandiza komanso kutonthoza mwauzimu anthu okhudzidwa ndi mphepo yamkuntho ya Irma ndi Maria.