Mboni za Yehova Padziko Lonse

Uruguay

  • Montevideo, Uruguay​—Akugawira kapepala kakuti, Kodi Mukuganiza Kuti Zinthu Zidzakhala Bwanji M’tsogolo?

Mfundo Zachidule—Uruguay

  • 3,506,000—Chiwerengero cha anthu
  • 12,000—Chiwerengero cha Mboni za Yehova
  • 149—Mipingo
  • Pa anthu 296 alionse pali wa Mboni za Yehova m’modzi