Mboni za Yehova Padziko Lonse

Ukraine

  • Lybokhora, Ukraine​—Akulalikira m’mudzi waung’ono

Mfundo Zachidule—Ukraine

  • 41,130,000—Chiwerengero cha anthu
  • 109,375—Chiwerengero cha Mboni za Yehova
  • 1,234—Mipingo
  • Pa anthu 391 alionse pali wa Mboni za Yehova m’modzi

KHALANI MASO

Nkhondo ya ku Ukraine Ikulowa Chaka Chachiwiri—Kodi Baibulo Limapereka Chiyembekezo Chotani?

Phunzirani zokhudza lonjezo lopezeka m’Baibulo lakuti nkhondo zonse zidzatha.

KHALANI MASO

Zimene Zipembedzo Zikuchita pa Nkhondo ya ku Ukraine—Kodi Baibulo Limanena Zotani?

Kumbali zonse, atsogoleri amatchalitchi ali ndi maganizo osiyana kwambiri ndi zomwe Yesu anaphunzitsa otsatira ake kuti azichita komanso zoti asamachite.