Mboni za Yehova Padziko Lonse

Trinidad and Tobago

Mfundo Zachidule—Trinidad and Tobago

  • 1,409,000—Chiwerengero cha anthu
  • 10,529—Chiwerengero cha Mboni za Yehova
  • 130—Mipingo
  • Pa anthu 135 alionse pali wa Mboni za Yehova m’modzi

NSANJA YA OLONDA (YOPHUNZIRA)

Makolo Anga Anandithandiza Kuti Ndizitumikira Yehova

Sangalalani ndi mbiri ya moyo wa Woodworth Mills, amene watumikira Yehova mokhulupirika kwa zaka pafupifupi 80.