Mboni za Yehova Padziko Lonse

Turkey

  • Istanbul, Turkey​—Akugawira magazini a Galamukani! a m’Chitekishi

Mfundo Zachidule—Turkey

  • 85,957,000—Chiwerengero cha anthu
  • 5,692—Chiwerengero cha Mboni za Yehova
  • 71—Mipingo
  • Pa anthu 15,502 alionse pali wa Mboni za Yehova m’modzi

NSANJA YA OLONDA (YOPHUNZIRA)

Anadzipereka ndi Mtima Wonse ku Turkey

Mu 2014, kunali ntchito yapadera yolalikira ku Turkey. N’chifukwa chiyani ntchito yapaderayi inachitika? Kodi zotsatirapo zake zinali zotani?