Mboni za Yehova Padziko Lonse

Turks and Caicos Islands

Mfundo Zachidule—Turks and Caicos Islands

  • 40,000—Chiwerengero cha anthu
  • 340—Chiwerengero cha Mboni za Yehova
  • 7—Mipingo
  • Pa anthu 122 alionse pali wa Mboni za Yehova m’modzi

NKHANI

A Mboni Akugwira Mwakhama Ntchito Yothandiza Anthu Omwe Anakhudzidwa Ndi Mphepo Zamkuntho

Maofesi a Nthambi a Mboni za Yehova akufotokoza zimene akuchita pothandiza komanso kutonthoza mwauzimu anthu okhudzidwa ndi mphepo yamkuntho ya Irma ndi Maria.