Mboni za Yehova Padziko Lonse

Swaziland

Mfundo Zachidule—Swaziland

  • 1,198,000—Chiwerengero cha anthu
  • 3,269—Chiwerengero cha Mboni za Yehova
  • 76—Mipingo
  • Pa anthu 377 alionse pali wa Mboni za Yehova m’modzi

NSANJA YA OLONDA (YOPHUNZIRA)

Mfumu Inasangalala Kwambiri

Werengani kuti mumve mmene mfumu ya ku Swaziland inkakondera kuphunzira Baibulo.