Mboni za Yehova Padziko Lonse

Saint Maarten

Mfundo Zachidule—Saint Maarten

  • 45,000—Chiwerengero cha anthu
  • 324—Chiwerengero cha Mboni za Yehova
  • 4—Mipingo
  • Pa anthu 149 alionse pali wa Mboni za Yehova m’modzi

NKHANI

A Mboni Akugwira Mwakhama Ntchito Yothandiza Anthu Omwe Anakhudzidwa Ndi Mphepo Zamkuntho

Maofesi a Nthambi a Mboni za Yehova akufotokoza zimene akuchita pothandiza komanso kutonthoza mwauzimu anthu okhudzidwa ndi mphepo yamkuntho ya Irma ndi Maria.