Mfundo Zachidule—El Salvador
- 6,582,000—Chiwerengero cha anthu
- 37,680—Chiwerengero cha Mboni za Yehova
- 607—Mipingo
- Pa anthu 176 alionse pali wa Mboni za Yehova m’modzi
GALAMUKANI!
Dziko la El Salvador
Werengani nkhaniyi kuti mudziwe zambiri za anthu ansangala a ku El Salvador.”