Mfundo Zachidule—Sierra Leone
- 8,472,000—Chiwerengero cha anthu
- 2,564—Chiwerengero cha Mboni za Yehova
- 42—Mipingo
- Pa anthu 3,621 alionse pali wa Mboni za Yehova m’modzi
NSANJA YA OLONDA (YOPHUNZIRA)
Zinthu Zinkayenda Bwino Chifukwa cha Chikondi
Ngati munayamba posachedwa kufika pa misonkhano ya Mboni za Yehova, mwina mungadabwe kudziwa zimene tinkachita kale.
BUKU LAPACHAKA LA MBONI ZA YEHOVA LA 2014
Sierra Leone ndi Guinea
Nkhaniyi ikusonyeza kuti Mboni za Yehova zakhala zikulalikira uthenga wabwino m’mayiko awiriwa mokhulupirika komanso modzipereka kwambiri.