Mboni za Yehova Padziko Lonse

Finland

  • Turku, Finland​—Akulalikira uthenga wa m’Baibulo

Mfundo Zachidule—Finland

  • 5,564,000—Chiwerengero cha anthu
  • 18,186—Chiwerengero cha Mboni za Yehova
  • 272—Mipingo
  • Pa anthu 307 alionse pali wa Mboni za Yehova m’modzi

NTCHITO YOLALIKIRA

Ntchito Yolalikira Mwapadera Inayenda Bwino ku Lapland

Onani zimene anthu a ku Lapland anachita pa ntchito yapadera imene a Mboni anagwira pofuna kuwathandiza.

NSANJA YA OLONDA (YOPHUNZIRA)

Tachita Utumiki wa Nthawi Zonse kwa Zaka 50 Kumpoto Kwenikweni

Werengani nkhani ya Aili ndi Annikki Mattila, omwe anaona ubwino wodalira Yehova pomwe ankatumikira ngati apainiya apadera ku kumpoto kwa dziko la Finland.