Mboni za Yehova Padziko Lonse

Rwanda

Mfundo Zachidule—Rwanda

  • 13,246,000—Chiwerengero cha anthu
  • 33,664—Chiwerengero cha Mboni za Yehova
  • 593—Mipingo
  • Pa anthu 418 alionse pali wa Mboni za Yehova m’modzi

NKHANI

Kukumbukira Nkhondo Yapachiweniweni Yomwe Inachitika ku Rwanda Zaka 25 Zapitazo

Wa Mboni za Yehova ku Rwanda akukumbukira chipwirikiti chomwe chinachitika pa nkhondo yapachiweniweni mu 1994 ndipo akufotokoza mmene chikondi chololera kuvutikira ena chinamupulumutsira.