Mboni za Yehova Padziko Lonse

Paraguay

  • Dera la Nueva Durango, Canindeyú, Paraguay​—Akugawira kabuku kakuti, Mverani Mulungu Kuti Mudzapeze Moyo Wosatha

Mfundo Zachidule—Paraguay

  • 7,391,000—Chiwerengero cha anthu
  • 11,042—Chiwerengero cha Mboni za Yehova
  • 186—Mipingo
  • Pa anthu 676 alionse pali wa Mboni za Yehova m’modzi