Mboni za Yehova Padziko Lonse

Papua New Guinea

  • Port Moresby, Papua New Guinea​—Akuwerenga vesi m’chinenero cha Chitoku Pisini

Mfundo Zachidule—Papua New Guinea

  • 9,466,000—Chiwerengero cha anthu
  • 5,692—Chiwerengero cha Mboni za Yehova
  • 89—Mipingo
  • Pa anthu 1,999 alionse pali wa Mboni za Yehova m’modzi

KALE LATHU

Boti la Lightbearer Linabweretsa Kuwala kwa Choonadi Kum’mwera Chakum’mawa kwa Asia

Ngakhale kuti ankatsutsidwa, amuna ochepa a m’boti la Lightbearer anafalitsa molimba mtima kuwala kwa choonadi cha m’Baibulo m’dera lalikulu kwambiri lokhala anthu ambiri.