Mfundo Zachidule—Panama
- 4,511,000—Chiwerengero cha anthu
- 18,525—Chiwerengero cha Mboni za Yehova
- 310—Mipingo
- Pa anthu 247 alionse pali wa Mboni za Yehova m’modzi
GALAMUKANI!
Panama
Ku Panama n’kotchuka kwambiri chifukwa cha ngalande zake. Werengani kuti mumve zambiri za anthu amene amkhala m’dziko limeneli.