Mfundo Zachidule—New Zealand
- 5,199,000—Chiwerengero cha anthu
- 14,607—Chiwerengero cha Mboni za Yehova
- 170—Mipingo
- Pa anthu 360 alionse pali wa Mboni za Yehova m’modzi
GALAMUKANI!
Dziko la New Zealand
Ngakhale kuti dziko New Zealand lili kutali kwambiri, alendo pafupifupi 3 miliyoni amalowa m’dzikoli. Kodi n’chiyani chimawachititsa chidwi alendowa?