Mboni za Yehova Padziko Lonse

Netherlands

Mfundo Zachidule—Netherlands

  • 17,878,000—Chiwerengero cha anthu
  • 29,584—Chiwerengero cha Mboni za Yehova
  • 346—Mipingo
  • Pa anthu 612 alionse pali wa Mboni za Yehova m’modzi

NSANJA YA OLONDA (YOPHUNZIRA)

Timasangalala Kutumikira Yehova Kwina Kulikonse

Werengani kuti mudziwe zimene banja lina la ku Netherlands lachita kuti lizikhulupirira Yehova ndi mtima wonse ngakhale kuti utumiki wawo unkasinthasintha komanso ankakumana ndi mavuto.