Mfundo Zachidule—Nicaragua
- 6,855,000—Chiwerengero cha anthu
- 28,843—Chiwerengero cha Mboni za Yehova
- 466—Mipingo
- Pa anthu 240 alionse pali wa Mboni za Yehova m’modzi
ZOCHITIKA PA MOYO
Madzi Osefukira Anabweretsa Uthenga Wabwino
Kutagwa mvula yamphamvu, anthu a ku Nicaragua anathandizidwa ndi anthu amene sankawayembekezera.
GALAMUKANI!
Dziko la Nicaragua
nyanja yopanda mchere momwe mumapezeka nsomba za m’nyanja zikuluzikulu monga shaki.