Mboni za Yehova Padziko Lonse

Nigeria

  • Idanre, Nigeria​—Akugawira magazini a Nsanja ya Olonda

Mfundo Zachidule—Nigeria

  • 222,182,000—Chiwerengero cha anthu
  • 400,375—Chiwerengero cha Mboni za Yehova
  • 6,071—Mipingo
  • Pa anthu 589 alionse pali wa Mboni za Yehova m’modzi

KODI ZOPEREKA ZANU ZIMAGWIRITSIDWA NTCHITO BWANJI?

Tchanelo cha JW Setilaiti Chimaoneka Kumene Kulibe Intaneti

Kodi abale a ku Africa amatani kuti aonere JW Broadcasting ngati alibe intaneti?

NSANJA YA OLONDA (YOPHUNZIRA)

Makolo Anga Anandithandiza Kuti Ndizitumikira Yehova

Sangalalani ndi mbiri ya moyo wa Woodworth Mills, amene watumikira Yehova mokhulupirika kwa zaka pafupifupi 80.

NTCHITO ZOMANGAMANGA

A Mboni za Yehova ku Nigeria Amanga Nyumba za Ufumu Zokwana 3,000

A Mboni za Yehova ku Nigeria anachita msonkhanowu pokumbukira kuti m’dzikoli mwamangidwa Nyumba za Ufumu 3,000. Pa mwambowu panafotokozedwa mbiri yachidule yokhudza ntchito ya a Mboni za Yehova m’dzikoli kuyambira m’ma 1920.