Mboni za Yehova Padziko Lonse

New Caledonia

  • Gombe la Anse Vata ku Nouméa, New Caledonia—Akukambirana ndi munthu pogwiritsa ntchito Baibulo

Mfundo Zachidule—New Caledonia

  • 271,000—Chiwerengero cha anthu
  • 2,693—Chiwerengero cha Mboni za Yehova
  • 34—Mipingo
  • Pa anthu 103 alionse pali wa Mboni za Yehova m’modzi

NKHANI

A Mboni za Yehova Anathandiza Anthu Okhudzidwa ndi Mphepo Yamkuntho

A Mboni za Yehova akuthandiza komanso kulimbikitsa anthu amene katundu wawo kapena nyumba zawo zinawonongeka ndi mphepo yoopsa.