Mboni za Yehova Padziko Lonse

Mozambique

  • Bairro dos Pescadores, pafupi ndi mzinda wa Maputo ku Mozambique​—Akugawira magazini a Nsanja ya Olonda

Mfundo Zachidule—Mozambique

  • 32,420,000—Chiwerengero cha anthu
  • 87,668—Chiwerengero cha Mboni za Yehova
  • 1,651—Mipingo
  • Pa anthu 398 alionse pali wa Mboni za Yehova m’modzi

KODI ZOPEREKA ZANU ZIMAGWIRITSIDWA NTCHITO BWANJI?

Kuonera Kapena Kumvetsera Msonkhano

Msonkhano wachigawo wa chaka cha 2020 unaikidwa pa intaneti, koma anthu ambiri ku Malawi ndi ku Mozambique sangakwanitse kugwiritsa ntchito intaneti. Ndiye kodi anatha bwanji kumvetsera msonkhanowu?