Mboni za Yehova Padziko Lonse

Malaysia

  • Tawuni ya George ku Malaysia—Akulalikira zokhudza Ufumu wa Mulungu

Mfundo Zachidule—Malaysia

  • 33,200,000—Chiwerengero cha anthu
  • 5,645—Chiwerengero cha Mboni za Yehova
  • 119—Mipingo
  • Pa anthu 5,959 alionse pali wa Mboni za Yehova m’modzi

KALE LATHU

Boti la Lightbearer Linabweretsa Kuwala kwa Choonadi Kum’mwera Chakum’mawa kwa Asia

Ngakhale kuti ankatsutsidwa, amuna ochepa a m’boti la Lightbearer anafalitsa molimba mtima kuwala kwa choonadi cha m’Baibulo m’dera lalikulu kwambiri lokhala anthu ambiri.