Mboni za Yehova Padziko Lonse

Mexico

  • Palacio de Bellas Artes, Mexico City, Mexico—Akuphunzitsa pogwiritsa ntchito Baibulo

  • Tauni ya Betania, m’dera la Chiapas, m’dziko la Mexico​—Akugawira kabuku kofotokoza Baibulo m’chilankhulo cha Chitsotsilu

  • Mzinda wa San Miguel de Allende, m’dera la Guanajuato, m’dziko la Mexico​—Akuwerengera munthu lemba lolimbikitsa la m’Baibulo

Mfundo Zachidule—Mexico

  • 132,834,000—Chiwerengero cha anthu
  • 864,738—Chiwerengero cha Mboni za Yehova
  • 12,706—Mipingo
  • Pa anthu 155 alionse pali wa Mboni za Yehova m’modzi

NSANJA YA OLONDA (YOPHUNZIRA)

“Kodi Tichitanso Liti Msonkhano Wina?”

N’chifukwa chiyani msonkhano wa mu 1932 wa ku Mexico City umene anthu 150 okha anapezeka ndi wosaiwalika?

NSANJA YA OLONDA (YOPHUNZIRA)

Anadzipereka ndi Mtima Wonse ku Mexico

Werengani kuti mumve kuti ndi achinyamata angati amene apirira mavuto osiyanasiyana ndi cholinga choti awonjezere zimene amachita mu utumiki.