Mboni za Yehova Padziko Lonse

Martinique

  • Pafupi ndi mzinda Sainte-Marie, ku Martinique​—Akuwerenga vesi lolimbikitsa m’Baibulo

Mfundo Zachidule—Martinique

  • 367,000—Chiwerengero cha anthu
  • 4,882—Chiwerengero cha Mboni za Yehova
  • 57—Mipingo
  • Pa anthu 76 alionse pali wa Mboni za Yehova m’modzi