Mboni za Yehova Padziko Lonse

Mongolia

  • Erdenet, Mongolia —Akukambirana pogwiritsa ntchito kabuku kofotokoza nkhani za m’Baibulo panja pa nyumba

Mfundo Zachidule—Mongolia

  • 3,423,000—Chiwerengero cha anthu
  • 432—Chiwerengero cha Mboni za Yehova
  • 8—Mipingo
  • Pa anthu 8,431 alionse pali wa Mboni za Yehova m’modzi

NKHANI

A Mboni za Yehova Awina Mlandu ku Mongolia Ndipo Alembetsanso Monga Chipembedzo Chovomerezeka ndi Boma

A Mboni za Yehova ku likulu la dziko la Mongolia anapatsidwa satifiketi yatsopano kuchokera ku ofesi yoyang’anira mzindawu yosonyeza kuti chipembedzo chawo n’chovomerezeka ndi boma.

GALAMUKANI!

Dziko la Mongolia

Moyo wa anthu ambiri ku Mongolia ndi wongoyendayenda koma amalandira bwino alendo.